Ezara 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho ine ndinalamula kuti afufuze, ndipo apeza kuti kuyambira kale mzinda umenewo wakhala ukuukira mafumu. Anthu amumzindawo akhala akuyambitsanso chisokonezo komanso kugalukira.+
19 Choncho ine ndinalamula kuti afufuze, ndipo apeza kuti kuyambira kale mzinda umenewo wakhala ukuukira mafumu. Anthu amumzindawo akhala akuyambitsanso chisokonezo komanso kugalukira.+