Ezara 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mʼchaka choyamba cha Koresi mfumu ya Babulo, mfumu Koresi inaika lamulo loti nyumba ya Mulunguyi imangidwenso.+
13 Koma mʼchaka choyamba cha Koresi mfumu ya Babulo, mfumu Koresi inaika lamulo loti nyumba ya Mulunguyi imangidwenso.+