Ezara 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koresiyo anamuuza kuti: “Tenga ziwiyazi, ukaziike mʼkachisi amene ali ku Yerusalemu. Ukaonetsetse kuti nyumba ya Mulungu yamangidwanso pamalo ake.”+
15 Koresiyo anamuuza kuti: “Tenga ziwiyazi, ukaziike mʼkachisi amene ali ku Yerusalemu. Ukaonetsetse kuti nyumba ya Mulungu yamangidwanso pamalo ake.”+