Ezara 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sezibazarayo atabwera anamanga maziko a nyumba ya Mulungu+ yomwe ili ku Yerusalemu. Kuyambira nthawi imeneyo mpaka pano nyumbayi ikumangidwabe ndipo sinamalizidwe.’+
16 Sezibazarayo atabwera anamanga maziko a nyumba ya Mulungu+ yomwe ili ku Yerusalemu. Kuyambira nthawi imeneyo mpaka pano nyumbayi ikumangidwabe ndipo sinamalizidwe.’+