Ezara 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu amene anaika dzina lake kumeneko,+ achotse mfumu iliyonse ndi anthu alionse ophwanya lamulo limeneli ndiponso owononga nyumba ya Mulungu imene ili ku Yerusalemu. Ine Dariyo ndaika lamulo limeneli, ndipo zichitike mwamsanga.”
12 Mulungu amene anaika dzina lake kumeneko,+ achotse mfumu iliyonse ndi anthu alionse ophwanya lamulo limeneli ndiponso owononga nyumba ya Mulungu imene ili ku Yerusalemu. Ine Dariyo ndaika lamulo limeneli, ndipo zichitike mwamsanga.”