Ezara 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje, Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita zimenezi mwamsanga mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 Nsanja ya Olonda,6/15/1993, tsa. 32
13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje, Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita zimenezi mwamsanga mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza.