-
Ezara 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Tsopano akuluakulu a Ayuda anapitiriza kumanga ndipo ntchitoyo inkayenda bwino+ chifukwa cholimbikitsidwa ndi ulosi wa mneneri Hagai+ ndi Zekariya+ mdzukulu wa Ido. Iwo anamanga nyumbayo nʼkuimaliza potsatira lamulo la Mulungu wa Isiraeli+ ndi lamulo la Koresi,+ Dariyo+ komanso Aritasasita mfumu ya Perisiya.+
-