Ezara 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena mwa Aisiraeli, ansembe, Alevi,+ oimba,+ alonda apageti+ ndi atumiki apakachisi*+ anapita ku Yerusalemu mʼchaka cha 7 cha mfumu Aritasasita. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:7 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 29
7 Ena mwa Aisiraeli, ansembe, Alevi,+ oimba,+ alonda apageti+ ndi atumiki apakachisi*+ anapita ku Yerusalemu mʼchaka cha 7 cha mfumu Aritasasita.