Ezara 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, iye ananyamuka kuchokera ku Babulo ndipo anafika ku Yerusalemu pa tsiku loyamba la mwezi wa 5. Iye anafika ku Yerusalemu chifukwa dzanja labwino la Mulungu wake linkamuthandiza.+ Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2136, 2244
9 Pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, iye ananyamuka kuchokera ku Babulo ndipo anafika ku Yerusalemu pa tsiku loyamba la mwezi wa 5. Iye anafika ku Yerusalemu chifukwa dzanja labwino la Mulungu wake linkamuthandiza.+