-
Ezara 7:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Zilizonse zimene iweyo ndi abale ako mudzaone kuti nʼzabwino kuchita ndi siliva ndi golide wotsala, mogwirizana ndi zimene Mulungu wanu akufuna, mudzachite zimenezo.
-