Ezara 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumʼpatse ngakhale matalente* 100 a siliva, miyezo ya kori* 100 ya tirigu, mitsuko* 100 ya vinyo,+ mitsuko 100 ya mafuta+ ndi mchere+ wambiri.
22 Mumʼpatse ngakhale matalente* 100 a siliva, miyezo ya kori* 100 ya tirigu, mitsuko* 100 ya vinyo,+ mitsuko 100 ya mafuta+ ndi mchere+ wambiri.