Ezara 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa ana a Adonikamu,+ omwe anali omaliza, panali anthu awa: Elifeleti, Yeyeli ndi Semaya. Iwo anali ndi amuna 60.
13 Pa ana a Adonikamu,+ omwe anali omaliza, panali anthu awa: Elifeleti, Yeyeli ndi Semaya. Iwo anali ndi amuna 60.