-
Ezara 8:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho ndinaitanitsa Eliezere, Ariyeli, Semaya, Elinatani, Yaribi, Elinatani, Natani, Zekariya ndi Mesulamu, omwe anali atsogoleri awo. Ndinaitanitsanso Yoyaribi ndi Elinatani, omwe anali alangizi.
-