Ezara 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuchokera pa atumiki apakachisi* amene Davide ndi akalonga anawaika kuti azitumikira Alevi, panali atumiki a pakachisi 220. Onsewa anawasankha pochita kuwatchula mayina awo.
20 Kuchokera pa atumiki apakachisi* amene Davide ndi akalonga anawaika kuti azitumikira Alevi, panali atumiki a pakachisi 220. Onsewa anawasankha pochita kuwatchula mayina awo.