Ezara 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho tinasala kudya nʼkupempha Mulungu wathu zimenezi ndipo iye anamva pempho lathu.+