Ezara 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Muyangʼanire katunduyu mosamala mpaka atayezedwa pamaso pa atsogoleri a ansembe, atsogoleri a Alevi komanso akalonga a nyumba zamakolo a Aisiraeli ku Yerusalemu,+ mʼzipinda zodyera zapanyumba ya Yehova.”
29 Muyangʼanire katunduyu mosamala mpaka atayezedwa pamaso pa atsogoleri a ansembe, atsogoleri a Alevi komanso akalonga a nyumba zamakolo a Aisiraeli ku Yerusalemu,+ mʼzipinda zodyera zapanyumba ya Yehova.”