Ezara 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako tinafika ku Yerusalemu+ ndipo tinakhala kumeneko masiku atatu.