-
Ezara 8:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Anthu amene anali ku ukapolo mʼdziko lina anapereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli. Anapereka ngʼombe zamphongo 12+ za Aisiraeli onse, nkhosa zamphongo 96,+ ana a nkhosa amphongo 77 ndi mbuzi zamphongo 12+ kuti zikhale nsembe yamachimo. Zonsezi anazipereka kuti zikhale nsembe zopsereza kwa Yehova.+
-