Ezara 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 amene munatilamula kudzera mwa atumiki anu aneneri, akuti, ‘Dziko limene mukukalitenga kuti likhale lanu ndi lodetsedwa chifukwa anthu ake ndi odetsedwa ndi zonyansa zawo zimene adzaza nazo dziko lonselo.+
11 amene munatilamula kudzera mwa atumiki anu aneneri, akuti, ‘Dziko limene mukukalitenga kuti likhale lanu ndi lodetsedwa chifukwa anthu ake ndi odetsedwa ndi zonyansa zawo zimene adzaza nazo dziko lonselo.+