Ezara 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene Ezara ankapemphera+ komanso kuvomereza machimo, zomwe ankachita akulira ndiponso atagona patsogolo pa nyumba ya Mulungu woona, gulu lalikulu la Aisiraeli linamuzungulira. Panali amuna, akazi ndi ana ndipo ankalira kwambiri.
10 Pamene Ezara ankapemphera+ komanso kuvomereza machimo, zomwe ankachita akulira ndiponso atagona patsogolo pa nyumba ya Mulungu woona, gulu lalikulu la Aisiraeli linamuzungulira. Panali amuna, akazi ndi ana ndipo ankalira kwambiri.