Ezara 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Ezara ananyamuka nʼkuuza atsogoleri a ansembe, a Alevi ndi a Aisiraeli onse kuti alumbire kuti achita mogwirizana ndi zimene ananena+ ndipo analumbiradi.
5 Choncho Ezara ananyamuka nʼkuuza atsogoleri a ansembe, a Alevi ndi a Aisiraeli onse kuti alumbire kuti achita mogwirizana ndi zimene ananena+ ndipo analumbiradi.