Ezara 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndipo mogwirizana ndi lamulo la akalonga ndi akulu, aliyense amene sabwera pakapita masiku atatu, katundu wake yense alandidwa ndipo iyeyo achotsedwa pa gulu la anthu amene anachokera ku ukapolo.+
8 ndipo mogwirizana ndi lamulo la akalonga ndi akulu, aliyense amene sabwera pakapita masiku atatu, katundu wake yense alandidwa ndipo iyeyo achotsedwa pa gulu la anthu amene anachokera ku ukapolo.+