-
Ezara 10:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho pasanathe masiku atatu, amuna onse a fuko la Yuda ndi la Benjamini anasonkhana ku Yerusalemu. Zimenezi zinachitika pa tsiku la 20 la mwezi wa 9. Anthu onsewo anakhala pabwalo la nyumba ya Mulungu woona, akunjenjemera chifukwa cha nkhaniyo komanso chifukwa kunkagwa mvula yambiri.
-