Ezara 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako wansembe Ezara anaimirira nʼkuuza anthuwo kuti: “Inu mwachita zosakhulupirika chifukwa mwatenga akazi achilendo+ ndipo mwawonjezera machimo a Isiraeli.
10 Kenako wansembe Ezara anaimirira nʼkuuza anthuwo kuti: “Inu mwachita zosakhulupirika chifukwa mwatenga akazi achilendo+ ndipo mwawonjezera machimo a Isiraeli.