-
Ezara 10:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma tilipo anthu ambiri ndipo ino ndi nyengo ya mvula, choncho nʼzosatheka kuima panja. Komanso nkhani imeneyi sitenga tsiku limodzi kapena masiku awiri chifukwa tachimwa kwambiri.
-