-
Ezara 10:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho lolani kuti akalonga athu aimire anthu onse+ ndipo aliyense mʼmizinda yathu, amene wakwatira mkazi wachilendo, abwere pa nthawi imene ikhazikitsidwe. Abwere limodzi ndi akulu a mzinda uliwonse ndi oweruza ake, mpaka titabweza mkwiyo wa Mulungu wathu amene watikwiyira kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.”
-