Ezara 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Yonatani mwana wa Asaheli ndi Yahazeya mwana wa Tikiva anatsutsa zimenezi, ndipo Mesulamu ndi Sabetai,+ omwe anali Alevi, anawathandiza.
15 Koma Yonatani mwana wa Asaheli ndi Yahazeya mwana wa Tikiva anatsutsa zimenezi, ndipo Mesulamu ndi Sabetai,+ omwe anali Alevi, anawathandiza.