-
Ezara 10:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Anthu amene anachokera ku ukapolowo anachita zimene anagwirizanazo. Choncho wansembe Ezara ndi amuna onse amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, omwe anachita kuwatchula mayina awo, anachoka pakati pa anthuwo nʼkukakhala pansi kuti afufuze nkhaniyo. Anachita zimenezi pa tsiku loyamba la mwezi wa 10.
-