-
Ezara 10:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pofika tsiku loyamba la mwezi woyamba, anathetsa nkhani zonse zokhudza amuna amene anatenga akazi achilendo.