Ezara 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anapeza kuti ana ena a ansembe anakwatira akazi achilendo.+ Kuchokera pa ana a Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ndi abale ake, panali Maaseya, Eliezere, Yaribi ndi Gedaliya.
18 Iwo anapeza kuti ana ena a ansembe anakwatira akazi achilendo.+ Kuchokera pa ana a Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ndi abale ake, panali Maaseya, Eliezere, Yaribi ndi Gedaliya.