Ezara 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iwo analonjeza kuti asiya akazi awo komanso popeza anachimwa, apereka nkhosa yamphongo chifukwa cha tchimo lawolo.+
19 Koma iwo analonjeza kuti asiya akazi awo komanso popeza anachimwa, apereka nkhosa yamphongo chifukwa cha tchimo lawolo.+