Nehemiya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako ndinafika kwa abwanamkubwa akutsidya lina la Mtsinje nʼkuwapatsa makalata a mfumu aja. Mfumu inandipatsanso akuluakulu a asilikali komanso asilikali okwera pamahatchi* kuti andiperekeze.
9 Kenako ndinafika kwa abwanamkubwa akutsidya lina la Mtsinje nʼkuwapatsa makalata a mfumu aja. Mfumu inandipatsanso akuluakulu a asilikali komanso asilikali okwera pamahatchi* kuti andiperekeze.