Nehemiya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atekowa+ anapitiriza kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa sanadzichepetse nʼkugwira nawo ntchito ya atsogoleri awo. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,7/2023, tsa. 7 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 102/15/1986, tsa. 25
5 Atekowa+ anapitiriza kuchokera pamene Zadoki analekezera. Koma anthu otchuka pakati pa Atekowa sanadzichepetse nʼkugwira nawo ntchito ya atsogoleri awo.
3:5 Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,7/2023, tsa. 7 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 102/15/1986, tsa. 25