Nehemiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoyada mwana wa Paseya, komanso Mesulamu mwana wa Besodeya, anakonza Geti la Mzinda Wakale.+ Iwo analipangira felemu lamatabwa nʼkuika zitseko, anamphatika* ndi mipiringidzo.
6 Yoyada mwana wa Paseya, komanso Mesulamu mwana wa Besodeya, anakonza Geti la Mzinda Wakale.+ Iwo analipangira felemu lamatabwa nʼkuika zitseko, anamphatika* ndi mipiringidzo.