Nehemiya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nehemiya mwana wa Azibuki, kalonga wa hafu ya chigawo cha Beti-zuri,+ anapitiriza kuchokera pamene Saluni analekezera. Anakafika patsogolo pa Manda Achifumu a Davide+ mpaka kudziwe+ lochita kukumba komanso ku Nyumba ya Anthu Amphamvu.
16 Nehemiya mwana wa Azibuki, kalonga wa hafu ya chigawo cha Beti-zuri,+ anapitiriza kuchokera pamene Saluni analekezera. Anakafika patsogolo pa Manda Achifumu a Davide+ mpaka kudziwe+ lochita kukumba komanso ku Nyumba ya Anthu Amphamvu.