Nehemiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ansembe, amuna amʼchigawo cha Yorodano*+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Meremoti analekezera.