-
Nehemiya 3:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Benjamini ndi Hasubu anakonza mpandawo kutsogolo kwa nyumba yawo kuchokera pamene ansembe analekezera. Azariya mwana wa Maaseya, mwana wa Ananiya, anakonza mpandawo pafupi ndi nyumba yake kuchokera pamene Benjamini ndi Hasubu analekezera.
-