Nehemiya 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Malikiya amene anali mʼgulu la osula golide, anakonza mpandawo kukafika kunyumba ya atumiki apakachisi*+ ndi amalonda, kutsogolo kwa Geti la Kufufuza mpaka pachipinda chapadenga chapakona.
31 Malikiya amene anali mʼgulu la osula golide, anakonza mpandawo kukafika kunyumba ya atumiki apakachisi*+ ndi amalonda, kutsogolo kwa Geti la Kufufuza mpaka pachipinda chapadenga chapakona.