-
Nehemiya 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iye anauza abale ake komanso asilikali a ku Samariya kuti: “Kodi Ayuda ofookawa akuchita chiyani? Kodi akuona ngati angaikwanitse ntchito imeneyi? Kodi adzapereka nsembe? Kodi amaliza kumangako tsiku limodzi? Kodi afukula miyala imene inatenthedwa nʼkukwiririka ndi dothi kuti aigwiritsenso ntchito?”+
-