-
Nehemiya 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma anthu a ku Yuda anayamba kunena kuti: “Mphamvu za anthu ogwira ntchito zatha, koma pali zinthu zambiri zofunika kuchotsa, ndipo sitingathe kumanga mpandawu.”
-