-
Nehemiya 4:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho ndinaika amuna kuseri kwa mpanda pamalo otsika omwe anali poonekera. Ndinawaika mogwirizana ndi mabanja awo atanyamula malupanga, mikondo ingʼonoingʼono ndi mauta.
-