Nehemiya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kungochokera tsiku limenelo, hafu ya anyamata anga ankagwira ntchito+ ndipo hafu inayo ankanyamula mikondo ingʼonoingʼono, zishango, mauta ndipo ankavala zovala za mamba achitsulo. Akalonga ankathandiza*+ anthu onse amʼnyumba ya Yuda
16 Kungochokera tsiku limenelo, hafu ya anyamata anga ankagwira ntchito+ ndipo hafu inayo ankanyamula mikondo ingʼonoingʼono, zishango, mauta ndipo ankavala zovala za mamba achitsulo. Akalonga ankathandiza*+ anthu onse amʼnyumba ya Yuda