Nehemiya 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiye mukamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, muzibwera kumene tili ndipo Mulungu wathu atimenyera nkhondo.”+
20 Ndiye mukamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, muzibwera kumene tili ndipo Mulungu wathu atimenyera nkhondo.”+