Nehemiya 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho ine, abale anga, atumiki anga+ ndi alonda amene ankanditsatira, sitinkasintha zovala ndipo aliyense ankanyamula mkondo mʼdzanja lake lamanja.
23 Choncho ine, abale anga, atumiki anga+ ndi alonda amene ankanditsatira, sitinkasintha zovala ndipo aliyense ankanyamula mkondo mʼdzanja lake lamanja.