-
Nehemiya 5:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ena ankanena kuti: “Ife ndi ana athu aamuna komanso aakazi tilipo ambiri. Tiyenera kupeza chakudya kuti tikhale ndi moyo.”
-