-
Nehemiya 5:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndipo ena ankanena kuti: “Nthawi ya njala, tikumapereka minda yathu ya tirigu, minda yathu ya mpesa ndi nyumba zathu monga chikole kuti tipeze chakudya.”
-