-
Nehemiya 6:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho ndinatumiza anthu kuti akawauze kuti: “Ntchito imene ndikugwirayi ndi yaikulu ndipo sindingathe kubwera. Kodi ntchitoyi iime chifukwa chakuti ine ndabwera kumeneko?”
-