-
Nehemiya 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Komanso waika aneneri kuti azilengeza za iwe mu Yerusalemu monse kuti, ‘Dziko la Yuda lili ndi mfumu!’ Mfumu ikhoza kumva mphekesera zimenezi. Choncho bwera tidzakambirane.”
-