-
Nehemiya 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako ndinapita kunyumba kwa Semaya mwana wa Delaya, mwana wa Mehetabele, amene anali atadzitsekera mʼnyumba. Iye anandiuza kuti: “Tiye tigwirizane nthawi yoti tikakumane kunyumba ya Mulungu woona, mʼkachisi ndipo tikatseke zitseko za kachisiyo. Chifukwa akubwera kudzakupha, akubwera kudzakupha usiku.”
-