Nehemiya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ntchito yomanga mpanda inatha pa tsiku la 25 la mwezi wa Eluli* ndipo inatenga masiku 52. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2142, 2244